Kampani yakatangale komaso yopepusa dziko la Malawi yatola chikwama ku KCH!

WhatsApp Video 2020-08-10 at 09.37.15

Kampani yomwe yapasidwa contract yoti iziyang’anila ndi kupanga supply zina ndi zina zofunikila pankhani ya Dialysis Department ku Kamuzu Central Hospital kwa zaka zitatu,pachaka chimodzi izilandila ndalama zosachepela $300,000.

Kampeni imeneyi kwa zaka zokwanila nkhumi ndi ziwili yakhala ikugwila ntchito mosayeneleka komanso mwa mwano ku Q.E.C.H,Aqueens akangochedwa kuwalipila ndalama amasiya kupeleka zofunikila kuchipatalako mpaka mapatient amatumizidwa ku KCH kwa iwo amalephela kupita ku Lilongwe kamba kosowa transport,amangozifela pankhomo.

Chaka chino akuluakulu aku queens akana kupanga renew contract ndi company imeneyi yopanda good custormer service or umunthu.

The Crooked Company.

It is strange the company has been given a huge contract whilst fully knowing their detestable personality. And the company is Germany based. The PPDA approved this while knowing that preference should go to local and similar service providers koma ayi akondwela kusankha kampani ya umbandayi.

Tawonani azanga kampani imeneyi inagwidwa ndi milandu yochita zachimphuphu mumayiko okwanili 13 mu africa muno.

Ndipo bungwe lalikuli lowona zamalamulo ku America ‘US Justice Department’ linawapatsa chindaputsa chokwanila $231 Million.

Read here:

https://www.justice.gov/opa/pr/fresenius-medical-care-agrees-pay-231-million-criminal-penalties-and-disgorgement-resolve

Welengani nkhani musimu.

The company is a kingpin of BRIBING THEIR WAY TO THE BANK TO COLLECT OUR TAXES AND IN RETURN GIVING US SHITTY SERVICES!.

#Observation

The Public Procurement and Disposal of Assets Authority(PPDA) must consider putting the awardment of this alleged fraudulent contract ON HOLD to investigate the fine details or if i were the Director of PPDA i would have advertised this contract in our daily newspapers to give chance to our local based companies with enough capacity to bid.

And the contract at Queens for Operating and servicing the Dialysis Department must be processed and let local based companies be prioritized.

That’s what our state president said, has been saying and he will continue to urge public institutions to give first preference to local companies and is within the PPDA ACT.

Let us adhere to RULE OF LAW.

Let us not sabotage the CHAKWERA’S ADMINISTRATION.

We can not give this sensitive and sentimental contract to a foreign based company that is nothing but a pure FRAUDSTER AND BRIBER!

I REPORT.

Yamikani Nicholas Kachingwe of Nazombe Village T/A Kapeni Blantyre.

Yamikani Kachingwe

Yamikani Nicholas Kachingwe is a Malawian with great interest in current affairs, news and storytelling. Over the years, he has established himself as a a great source of news, a private investigator of issues and whistle blower using various social media platforms.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *