TSIKANA WAWOLA KATUNDU YENSE NDI KUTHAWA

By Simon Petulo

Mnyamata wina kwa MANJE mumzinda wa BLANTYRE,manja ali kunkhongo HULE yemwe anagona naye mnyumba,atamukwangula K18,000 komaso ufa wonse ndi ndiwo zomwe adagula.

Nkhaniyo ikuti pa 05 February Chaka chino,mnyamatayu yemwe ndi Simoni Kaisa wadzaka 34,adapita ku malo ena womwera mowa.Ndipo ali komweko,adapeza hule ndikupita naye kunyumba kwake.

Anthuwa,ali komweko adakambirana zomanga banja.

Mwamunayu,akapita ku ntchito,amamusiyira mkaziyu zofunika zonse.

Lero wakhumudwa mkaziyo,atawola zakudya zonse komaso ndalama yomwe adasunga kuti achite transport yokawonekera kwa mkaziyo ku SALIMA.

Yamikani Kachingwe

Yamikani Nicholas Kachingwe is a Malawian with great interest in current affairs, news and storytelling. Over the years, he has established himself as a a great source of news, a private investigator of issues and whistle blower using various social media platforms.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *