SALIMA: TRANSFORMER AYINYANYALA A ESCOM

WhatsApp Video 2020-08-10 at 09.37.15

By Ebenezer

Transformer ya ESCOM yomwe pa 1/2/2020 idagwa koma mpakanalero a ESCOM sanadzatengebe or kuyikhonza, adangobwera ndikuzaiona nkuisiya pomwepo.

Mwakuti mvula yonseyi iripamatope,naye oil akungotuluka moti mawaya ena ali ndi moto , chimene chikuwophyesa anthu maka masiku.

Mmene mukoneramo uku ndi SALIMA ku NGODZI pa Chipatara cha Lifeline.
Akuluakulu a Chipatalachi akuti adapeleka vututoli ku ESCOM ndi ku BOMA kudzela kwa district Health officer wa Bomalo, koma sizikuthandiza.

Moti Odwala oyembekezera akuchirira mu Mdima kamba ka vutoli izi zakhudza anthu ambiri omwe anadalira Magetsi m’deralo.

Yamikani Kachingwe

Yamikani Nicholas Kachingwe is a Malawian with great interest in current affairs, news and storytelling. Over the years, he has established himself as a a great source of news, a private investigator of issues and whistle blower using various social media platforms.

18 thoughts on “SALIMA: TRANSFORMER AYINYANYALA A ESCOM

Comments are closed.