NGOZI YOOPSA PA MPINGU:ANTHU AWIRI AMWALIRA

WhatsApp Video 2020-08-10 at 09.37.15

Pachitika ngozi yoopsa pa Mpingu trading centre pomwe anthu awiri aferatu pa malo angozi.

Galimoto la black la mtundu wa Note limachokera kwa Nakuwawa mseu opita ku Nsaru kupita kuchipatala ndi odwala.

Pamene limalowa mu Mseu wa mchinji linakumana ndi ngozi imene lorry inagunda ka galimoto kakang’ono koyera mu chithuzi.
Poti athawire mbali inayi wapezeka wakalowa kupasi kwa lorry.

Ndiye driver kapena kuti oyendetsa wafera pompo pamodzi ndi munthu amene anakwera kutsogolo. Odwala ndi anthu ena awiri avulala modetsa nkhawa ndipo ali ku chipatala.

Yamikani Kachingwe

Yamikani Nicholas Kachingwe is a Malawian with great interest in current affairs, news and storytelling. Over the years, he has established himself as a a great source of news, a private investigator of issues and whistle blower using various social media platforms.

4 thoughts on “NGOZI YOOPSA PA MPINGU:ANTHU AWIRI AMWALIRA

 • May 21, 2020 at 9:31 am
  Permalink

  Hi there are using WordPress for your blog platform? I’m new to the blog world but I’m trying to get started and set up my own. Do you need any coding expertise to make your own blog? Any help would be greatly appreciated!

 • August 10, 2020 at 2:56 am
  Permalink

  Hi there all, here every one is sharing such familiarity, so it’s good
  to read this weblog, and I used to pay a visit this web site everyday.

 • August 10, 2020 at 3:20 am
  Permalink

  Paragraph writing is also a excitement, if you know after that you can write or else it is complicated to
  write.

 • August 14, 2020 at 12:51 am
  Permalink

  Greetings! I’ve been reading your site for some time now and finally got the courage
  to go ahead and give you a shout out from New Caney Texas!
  Just wanted to say keep up the great work!

Comments are closed.