LAMYA YAMANJA YAPHETSA MUNTHU.

Bambo wina ku Mzimba anatenga phone ya mlongo wake nkukaigulisa; kumfunsa anakana.

Phone inapezeka m’mudzi momwemo patadutsa masiku asanu ndiawiri.

Kumfunsa ogulayo anawatchula bambowa.

Kenako atadzudzulidwa chifukwa cha khalidwe lawolo, anangosowapo pakhomopo.

Anazapezeka atazimangilira mu mtengo wa mango pa katchire pena mmudzi momwemo dzulo.

Zimenezi zachitika dzulo masana.

Zambili zibwelabe,tikalandila report kuchokela ku police.

Yamikani Kachingwe

Yamikani Nicholas Kachingwe is a Malawian with great interest in current affairs, news and storytelling. Over the years, he has established himself as a a great source of news, a private investigator of issues and whistle blower using various social media platforms.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *