BAMBO WANYERE YOSAVUKA,WAGWILIRA MAYI AKE OBALA KOMASO KUWAPHA

Dzulo laliwisi lomweli mkulu wina amakhala kwa Phalula ku Balaka anamenya mayi wawo owabereka enieni ndi Mpini wa khasu ndi kuwagona.

Kuphatikiza kuwapanga zonsezo iye anawapha.

Kupanda kupulumusidwa ndi a Police; anthu okwiya amafuna kumuwotcha wamoyo.

Ndipo anthu mdelaro a dzudzula apolice-wo polanditsa munthu oyipitsitsayu ndipo a lonjeza kuti adzakamutulutsa mwachangu adzamuphabe pamene ena akuti tikangowotcha police station.

Pakali pano munthuyo akusungidwa ku Balaka police station.

Yamikani Kachingwe

Yamikani Nicholas Kachingwe is a Malawian with great interest in current affairs, news and storytelling. Over the years, he has established himself as a a great source of news, a private investigator of issues and whistle blower using various social media platforms.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *