ACHOTSANA CHALA CHIFUKWA CHOKAN GANILANA SHEIK BAMUSI

WhatsApp Video 2020-08-10 at 09.37.15

CAPE TOWN – CAPE FLATS (05)

Atsikana awiri Aisha ndi Nelie awumbuzana ku ku Cape Town Sabata lathali chifukwa cholimbanilana Mamuna.

Aisha wavala chofiilayo anali Mamuna wa Sheik Bamusi koma anamuthamangitsa mamunayi pa zifukwa zosadxiwika bwino.Chiipa uli nacho ,mauwa anathandauzira moyo wa Aisha kutapezeka kuti mamunayo akudyana ndi tsikana wina dera la Athlone Crawford yemwe ali Nelie,motero awiriwa akhala akumenyana kokwana kasanu akakumana ku Crawford komwe onsewa amatengera Sitima popita ku ntchito.

Chinali chindewu , kuumbuzana mene achitira azimai akwa Sundwe,mene tikunena pano Aisha yemwe ali MG 1 watupa mutu komaso Chala chinasala pang’ono kuduka mano a MG 2 Nelie ataluma ndikunyenya mochititsa mantha.

Pano MG 2 Nelie walanda Mamuna, Aisha wakhomera chinkhoswe,tsiku lomwelo la ndeuyi Sheik anakaswa Bwanda kwa Nelie.

Chodetsa nkhawa choti azimai onsewa akumaenda ndi mipeni kuti angothana pano komanso Nelie watapidwa phazi ndi Aisha kuti mwina angomuonetsa zachikhalidwe chathu.

LANGIZO:

Mamuna akamapanga za uhule njira yabwino ingosokesani moonekera ndi munthu omudziwa mukatero mwamupatsa mwambo.

ATAKHALE NDI MOYO AONA ZINTHU.

12 thoughts on “ACHOTSANA CHALA CHIFUKWA CHOKAN GANILANA SHEIK BAMUSI

Comments are closed.